2 Samueli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Yowabu anafunsa Amasa kuti: “Kodi zili bwino m’bale wanga?”+ Kenako dzanja lamanja la Yowabu linagwira ndevu za Amasa kuti amupsompsone.+ Mateyu 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+ Luka 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+
9 Ndiyeno Yowabu anafunsa Amasa kuti: “Kodi zili bwino m’bale wanga?”+ Kenako dzanja lamanja la Yowabu linagwira ndevu za Amasa kuti amupsompsone.+
34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+
47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+