Ekisodo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi m’buku monga chikumbutso+ ndi kumuuza Yoswa kuti, ‘M’kupita kwa nthawi ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi* ndipo sadzakumbukika n’komwe.’”+ 1 Samueli 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atachoka, Sauli anapha Aamaleki+ kuyambira ku Havila+ mpaka ku Shura,+ kufupi ndi Iguputo. 2 Samueli 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inapatula siliva ndi golide wochokera ku Siriya, Mowabu,+ kwa ana a Amoni, Afilisiti,+ Aamaleki+ ndiponso siliva ndi golide amene anafunkha kwa Hadadezeri mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba.+
14 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi m’buku monga chikumbutso+ ndi kumuuza Yoswa kuti, ‘M’kupita kwa nthawi ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi* ndipo sadzakumbukika n’komwe.’”+
12 Inapatula siliva ndi golide wochokera ku Siriya, Mowabu,+ kwa ana a Amoni, Afilisiti,+ Aamaleki+ ndiponso siliva ndi golide amene anafunkha kwa Hadadezeri mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba.+