Genesis 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Leya anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamutcha Rubeni,*+ popeza anati: “N’chifukwa chakuti Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda kwambiri.”
32 Kenako Leya anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamutcha Rubeni,*+ popeza anati: “N’chifukwa chakuti Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda kwambiri.”