Nehemiya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano akalonga+ a anthuwo anali kukhala m’Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi mwa anthu 10 alionse woti akakhale m’Yerusalemu, mzinda woyera,+ ndiponso kuti anthu ena 9 otsalawo akhale m’mizinda ina. Ezekieli 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzawaphatikiza kuti akhale mtundu umodzi m’dzikolo,+ m’mapiri a Isiraeli. Onsewo adzakhala ndi mfumu imodzi+ ndipo sadzakhalanso mitundu iwiri kapena kugawanika kukhala maufumu awiri.+ Hoseya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo ana a Yuda ndi ana a Isiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzadziikira mtsogoleri mmodzi ndi kutuluka m’dzikolo,+ chifukwa tsikuli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.*+
11 Tsopano akalonga+ a anthuwo anali kukhala m’Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi mwa anthu 10 alionse woti akakhale m’Yerusalemu, mzinda woyera,+ ndiponso kuti anthu ena 9 otsalawo akhale m’mizinda ina.
22 Ndidzawaphatikiza kuti akhale mtundu umodzi m’dzikolo,+ m’mapiri a Isiraeli. Onsewo adzakhala ndi mfumu imodzi+ ndipo sadzakhalanso mitundu iwiri kapena kugawanika kukhala maufumu awiri.+
11 Pamenepo ana a Yuda ndi ana a Isiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzadziikira mtsogoleri mmodzi ndi kutuluka m’dzikolo,+ chifukwa tsikuli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.*+