1 Mafumu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mkulu wa asilikali,+ ndipo Zadoki ndi Abiyatara+ anali ansembe. 1 Mbiri 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtsogoleri wa gulu lachitatu, lotumikira mwezi wachitatu, anali Benaya+ mwana wa Yehoyada+ wansembe wamkulu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
5 Mtsogoleri wa gulu lachitatu, lotumikira mwezi wachitatu, anali Benaya+ mwana wa Yehoyada+ wansembe wamkulu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.