2 Samueli 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti wamukwezera+ ufumu wake chifukwa cha anthu ake Aisiraeli.+ Salimo 89:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Dzanja langa lolimba lidzakhala pa iye.+Mkono wanga udzamulimbitsa.+
12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti wamukwezera+ ufumu wake chifukwa cha anthu ake Aisiraeli.+