2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 1 Mbiri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike+ mu Isiraeli, pakuti ufumu wake unakwezedwa kwambiri chifukwa cha anthu ake Aisiraeli.+ Salimo 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+ Salimo 89:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Dzanja langa lolimba lidzakhala pa iye.+Mkono wanga udzamulimbitsa.+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
2 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike+ mu Isiraeli, pakuti ufumu wake unakwezedwa kwambiri chifukwa cha anthu ake Aisiraeli.+
11 Mukatero ndidziwa kuti mwasangalala nane,Chifukwa mdani wanga sadzafuula mosangalala kuti wandipambana.+