Numeri 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Madzi odzaza mitsuko yake iwiri akutayikirabe pansi,Ndipo mbewu yake ili m’mbali mwa madzi ambiri.+Mfumu yakenso+ idzakwezeka kuposa Agagi,+Ndi ufumu wake udzakwezedwa.+ 2 Samueli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli. 1 Mafumu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wasangalala+ nanu mwa kukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli.+ Popeza Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale,+ wakuikani kuti mukhale mfumu+ kuti muzipereka zigamulo+ ndi kuchita chilungamo.”+
7 Madzi odzaza mitsuko yake iwiri akutayikirabe pansi,Ndipo mbewu yake ili m’mbali mwa madzi ambiri.+Mfumu yakenso+ idzakwezeka kuposa Agagi,+Ndi ufumu wake udzakwezedwa.+
8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli.
9 Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wasangalala+ nanu mwa kukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli.+ Popeza Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale,+ wakuikani kuti mukhale mfumu+ kuti muzipereka zigamulo+ ndi kuchita chilungamo.”+