-
2 Samueli 23:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mulungu wa Isiraeli analankhula,
Thanthwe la Isiraeli linandiuza kuti,+
‘Munthu wolamulira anthu akakhala wolungama,+
N’kumalamulira moopa Mulungu,+
-