Deuteronomo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+ 1 Mbiri 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inutu munapanga anthu anu Aisiraeli kuti akhaledi anthu anu+ mpaka kalekale. Ndipo inu Yehova munakhala Mulungu wawo.+ 2 Mbiri 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Hiramu mfumu ya Turo+ atamva, analemba kalata ndi kuitumiza kwa Solomo, kuti: “Popeza kuti Yehova anakonda+ anthu ake, waika inu kukhala mfumu yawo.”+
8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+
22 Inutu munapanga anthu anu Aisiraeli kuti akhaledi anthu anu+ mpaka kalekale. Ndipo inu Yehova munakhala Mulungu wawo.+
11 Hiramu mfumu ya Turo+ atamva, analemba kalata ndi kuitumiza kwa Solomo, kuti: “Popeza kuti Yehova anakonda+ anthu ake, waika inu kukhala mfumu yawo.”+