Deuteronomo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+ Deuteronomo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye analinso kukonda anthu ake.+Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+
8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu+ kuti akulanditseni m’nyumba yaukapolo,+ m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani,+ komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+
3 Iye analinso kukonda anthu ake.+Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+