1 Mafumu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wasangalala+ nanu mwa kukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli.+ Popeza Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale,+ wakuikani kuti mukhale mfumu+ kuti muzipereka zigamulo+ ndi kuchita chilungamo.”+ 2 Mbiri 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Hiramu mfumu ya Turo+ atamva, analemba kalata ndi kuitumiza kwa Solomo, kuti: “Popeza kuti Yehova anakonda+ anthu ake, waika inu kukhala mfumu yawo.”+
9 Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wasangalala+ nanu mwa kukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli.+ Popeza Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale,+ wakuikani kuti mukhale mfumu+ kuti muzipereka zigamulo+ ndi kuchita chilungamo.”+
11 Hiramu mfumu ya Turo+ atamva, analemba kalata ndi kuitumiza kwa Solomo, kuti: “Popeza kuti Yehova anakonda+ anthu ake, waika inu kukhala mfumu yawo.”+