Salimo 104:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mumapanga angelo anu kukhala mizimu,+Ndipo atumiki anu kukhala moto wonyeketsa.+ Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amapanga angelo ake kukhala mizimu, ndipo amapanganso antchito ake otumikira ena kukhala lawi la moto.”+