Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+ 1 Mafumu 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Yehova waika mzimu wabodza m’kamwa mwa aneneri anu onsewa,+ koma Yehovayo wanena kuti inuyo muona tsoka.”+ Ezekieli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo ukachenjeza munthu woipa,+ koma iye osasiya zoipa zakezo ndi njira zake zoipa, munthuyo adzafa chifukwa cha zoipa zake.+ Koma iweyo udzakhala utapulumutsa moyo wako.+
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
23 Choncho Yehova waika mzimu wabodza m’kamwa mwa aneneri anu onsewa,+ koma Yehovayo wanena kuti inuyo muona tsoka.”+
19 Koma iweyo ukachenjeza munthu woipa,+ koma iye osasiya zoipa zakezo ndi njira zake zoipa, munthuyo adzafa chifukwa cha zoipa zake.+ Koma iweyo udzakhala utapulumutsa moyo wako.+