Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+

      Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+

      Kodi ananenapo kanthu koma osachita,

      Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+

  • 1 Mafumu 20:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+

  • 2 Mbiri 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Choncho Yehova waika mzimu wabodza m’kamwa mwa aneneri anuwa,+ koma Yehovayo wanena kuti inuyo muona tsoka.”+

  • Yesaya 55:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena