Yesaya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+ Ezekieli 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Ngati mneneri wapusitsidwa n’kulankhula mawu, ineyo Yehova ndi amene ndamupusitsa mneneriyo.+ Ndidzamutambasulira dzanja langa n’kumuwononga pakati pa anthu anga, Aisiraeli.+
14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+
9 “‘Ngati mneneri wapusitsidwa n’kulankhula mawu, ineyo Yehova ndi amene ndamupusitsa mneneriyo.+ Ndidzamutambasulira dzanja langa n’kumuwononga pakati pa anthu anga, Aisiraeli.+