2 Mafumu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pomalizira pake Yehu anafika ku Samariya. Kumeneko, iye anapha anthu onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Samariya, mpaka anawatha onse,+ mogwirizana ndi mawu a Yehova amene anauza Eliya.+
17 Pomalizira pake Yehu anafika ku Samariya. Kumeneko, iye anapha anthu onse a m’nyumba ya Ahabu amene anatsala ku Samariya, mpaka anawatha onse,+ mogwirizana ndi mawu a Yehova amene anauza Eliya.+