8 Nyumba yonse ya Ahabu+ ifafanizidwe. Ine ndidzapha munthu aliyense wokodzera khoma*+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale aliyense wonyozeka ndi wopanda pake+ mu Isiraeli.
7 Koma Mulungu ndi amene anachititsa+ kuti Ahaziya awonongeke+ mwa kupita kwa Yehoramu. Atafika kumeneko, anatengana+ ndi Yehoramu n’kupita kukakumana ndi Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ yemwe Yehova anam’dzoza+ kuti aphe a m’nyumba ya Ahabu.+