21 ndikubweretsera tsoka+ ndipo ndithu ndidzaseseratu nyumba yako,+ ndi kupha munthu aliyense wokodzera khoma+ wa m’banja la Ahabu, ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake mu Isiraeli.
26 ‘“Ndithu magazi+ a Naboti ndi magazi a ana ake+ amene ndawaona dzulo,” watero Yehova, “ndidzawabwezera+ pa iwe ndithu m’munda uwu,” Yehova watero.’ Choncho munyamule, umuponye m’mundamo mogwirizana ndi mawu a Yehova.”+