1 Mbiri 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anawagawa m’magulu+ ndi kuwapereka kwa ana a Levi.+ Anawapereka kwa Gerisoni, Kohati, ndi Merari. 1 Mbiri 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Analinso kutumikira m’mawa ulionse+ pa nthawi yoimirira+ kuti athokoze+ ndi kutamanda+ Yehova. Analinso kuchita zimenezi madzulo.
6 Ndiyeno Davide anawagawa m’magulu+ ndi kuwapereka kwa ana a Levi.+ Anawapereka kwa Gerisoni, Kohati, ndi Merari.
30 Analinso kutumikira m’mawa ulionse+ pa nthawi yoimirira+ kuti athokoze+ ndi kutamanda+ Yehova. Analinso kuchita zimenezi madzulo.