1 Mafumu 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iye anali wanzeru kuposa munthu wina aliyense. Anali wanzeru kuposa Etani+ mwana wa Zera, Hemani,+ Kalikoli,+ ndi Darida ana a Maholi. Ndipo anatchuka m’mitundu yonse yozungulira.+
31 Iye anali wanzeru kuposa munthu wina aliyense. Anali wanzeru kuposa Etani+ mwana wa Zera, Hemani,+ Kalikoli,+ ndi Darida ana a Maholi. Ndipo anatchuka m’mitundu yonse yozungulira.+