2 Mbiri 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pobwerera kuchokera kokapha Aedomu, Amaziya anatenga milungu+ ya ana a Seiri n’kukaiimika kuti ikhale milungu yake.+ Kenako anayamba kuigwadira+ ndi kuifukizira nsembe yautsi.+ Yeremiya 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma inu simunamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti musiye kuchita zinthu zoipa zomwe ndi kupereka nsembe zautsi kwa milungu ina.+
14 Koma pobwerera kuchokera kokapha Aedomu, Amaziya anatenga milungu+ ya ana a Seiri n’kukaiimika kuti ikhale milungu yake.+ Kenako anayamba kuigwadira+ ndi kuifukizira nsembe yautsi.+
5 Koma inu simunamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti musiye kuchita zinthu zoipa zomwe ndi kupereka nsembe zautsi kwa milungu ina.+