2 Mbiri 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 M’mizinda yonse ya Yuda anamangamo malo okwezeka+ operekera nsembe zautsi kwa milungu ina.+ Chotero anakwiyitsa+ Yehova Mulungu wa makolo ake. 2 Mbiri 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 chifukwa chakuti andisiya+ n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho nditsanulira mkwiyo wanga+ pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+
25 M’mizinda yonse ya Yuda anamangamo malo okwezeka+ operekera nsembe zautsi kwa milungu ina.+ Chotero anakwiyitsa+ Yehova Mulungu wa makolo ake.
25 chifukwa chakuti andisiya+ n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse+ ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho nditsanulira mkwiyo wanga+ pamalo ano ndipo suzimitsidwa.’”+