Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndipo nawonso anapitiriza kudzimangira malo okwezeka,+ zipilala zopatulika,+ ndi mizati yopatulika+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali,+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+

  • 2 Mafumu 15:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo. Iye ndiye anamanga chipata chakumtunda cha nyumba ya Yehova.+

  • 2 Mbiri 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Komanso iye anamanga malo okwezeka+ m’mapiri a ku Yuda kuti achititse anthu okhala mu Yerusalemu kuchita zoipa,+ ndiponso kuti asocheretse Yuda.+

  • 2 Mbiri 33:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho iye anamanganso malo okwezeka+ amene Hezekiya bambo ake anagwetsa.+ Anamanga maguwa ansembe+ a Abaala+ n’kumanga mizati yopatulika,+ ndipo anayamba kugwadira+ khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ n’kumazitumikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena