Oweruza 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ana a Isiraeli anayamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova,+ n’kuyamba kutumikira Abaala.+ 2 Mbiri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anayenda m’njira za mafumu a Isiraeli,+ ndipo anafika mpaka popangira Abaala+ zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula.+
11 Ndiyeno ana a Isiraeli anayamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova,+ n’kuyamba kutumikira Abaala.+
2 Koma anayenda m’njira za mafumu a Isiraeli,+ ndipo anafika mpaka popangira Abaala+ zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula.+