27 Gawo lawolo linaphatikizaponso mizinda ya m’chigwa ya Beti-harana,+ Beti-nimira,+ Sukoti,+ Zafoni, ndi mbali yotsala ya dziko la Sihoni mfumu ya Hesiboni.+ Mtsinje wa Yorodano ndiwo unali malire awo mpaka kunyanja ya Kinereti.+ Gawo lawo linali kum’mawa kwa mtsinje wa Yorodano.