Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Pali milungu 70 imene yaikidwa yokhudza anthu a mtundu wako+ ndi mzinda wanu woyera,+ ndi cholinga choti athetse kuphwanya malamulo,+ athetse machimo,+ aphimbe cholakwa,+ abweretse chilungamo kuti chikhalepo mpaka kalekale,+ adinde chidindo+ pa masomphenya ndi maulosi, ndiponso kuti adzoze Malo Opatulikitsa.+

  • Akolose 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kuti kudzera mwa mwana wakeyo iye agwirizanitsenso+ zinthu zina zonse ndi iyeyo,+ pokhazikitsa mtendere+ mwa magazi+ amene iye anakhetsa pamtengo wozunzikirapo,*+ kaya zikhale zinthu zapadziko lapansi kapena zinthu zakumwamba.

  • 1 Yohane 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena