Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 31:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena m’bale wake+ kuti, ‘Mum’dziwe Yehova!’+ pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu,”+ watero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+

  • Luka 1:77
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 77 Kukadziwitsa anthu ake za chipulumutso pokhululukidwa machimo awo,+

  • Aroma 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Inde, popeza munamasulidwa+ ku uchimo, munakhala akapolo+ a chilungamo.+

  • Aheberi 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Zikanatero, akanavutika mobwerezabwereza kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa.+ Koma tsopano iye waonekera+ kamodzi+ kokha pa mapeto a nthawi* zino+ kuti achotse uchimo kudzera mu nsembe yake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena