Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa kusunga masabata a Yehova,+ kupereka mphatso zanu,+ nsembe zanu zonse za lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene muyenera kupereka kwa Yehova.
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa kusunga masabata a Yehova,+ kupereka mphatso zanu,+ nsembe zanu zonse za lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene muyenera kupereka kwa Yehova.