Yoswa 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Fuko la Manase linapatsidwa magawo 10, kuwonjezera pa dera la Giliyadi ndi Basana lomwe linali kutsidya lina la Yorodano.+ Yoswa 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Malire a gawo la fuko la Manase anayambira ku Aseri kukafika ku Mikametatu,+ patsogolo pa Sekemu.+ Malirewo analowera kumanja kukafika kwa anthu okhala ku Eni-Tapuwa. 2 Mbiri 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu+ ochokera ku Aseri, ku Manase, ndi ku Zebuloni okha ndi amene anadzichepetsa+ n’kubwera ku Yerusalemu.
5 Fuko la Manase linapatsidwa magawo 10, kuwonjezera pa dera la Giliyadi ndi Basana lomwe linali kutsidya lina la Yorodano.+
7 Malire a gawo la fuko la Manase anayambira ku Aseri kukafika ku Mikametatu,+ patsogolo pa Sekemu.+ Malirewo analowera kumanja kukafika kwa anthu okhala ku Eni-Tapuwa.
11 Anthu+ ochokera ku Aseri, ku Manase, ndi ku Zebuloni okha ndi amene anadzichepetsa+ n’kubwera ku Yerusalemu.