Ekisodo 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chotero Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Lamulo la pasika ndi ili:+ Mlendo* asadye nawo.+ Levitiko 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova. 2 Mbiri 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako Yosiya+ anachita pasika+ wa Yehova ku Yerusalemu, ndipo iwo anapha nyama ya pasika+ pa tsiku la 14+ la mwezi woyamba.+ 1 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+
5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova.
35 Kenako Yosiya+ anachita pasika+ wa Yehova ku Yerusalemu, ndipo iwo anapha nyama ya pasika+ pa tsiku la 14+ la mwezi woyamba.+
7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+