2 Mbiri 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu+ ochokera ku Aseri, ku Manase, ndi ku Zebuloni okha ndi amene anadzichepetsa+ n’kubwera ku Yerusalemu. 2 Mbiri 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Panali anthu ambiri ochokera ku Efuraimu,+ ku Manase,+ ku Isakara ndi ku Zebuloni+ amene sanadziyeretse+ ndipo anadya pasikayo mosatsatira zimene zinalembedwa.+ Koma Hezekiya anawapempherera+ kuti: “Yehova wabwino+ asakwiyire
11 Anthu+ ochokera ku Aseri, ku Manase, ndi ku Zebuloni okha ndi amene anadzichepetsa+ n’kubwera ku Yerusalemu.
18 Panali anthu ambiri ochokera ku Efuraimu,+ ku Manase,+ ku Isakara ndi ku Zebuloni+ amene sanadziyeretse+ ndipo anadya pasikayo mosatsatira zimene zinalembedwa.+ Koma Hezekiya anawapempherera+ kuti: “Yehova wabwino+ asakwiyire