Genesis 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zitatero, Isaki anayamba kubzala mbewu m’dzikomo.+ M’chaka chimenechi anakolola zochuluka moti pa mbewu zimene anabzala, anakolola zochuluka kuwirikiza nthawi 100,+ popeza Yehova anali kum’dalitsa.+ Levitiko 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Dziwani kuti ndidzakudalitsani m’chaka cha 6, ndipo dzikolo lidzakupatsani chakudya cha zaka zitatu.+ Miyambo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa,+ ndipo sawonjezerapo ululu.+
12 Zitatero, Isaki anayamba kubzala mbewu m’dzikomo.+ M’chaka chimenechi anakolola zochuluka moti pa mbewu zimene anabzala, anakolola zochuluka kuwirikiza nthawi 100,+ popeza Yehova anali kum’dalitsa.+
21 Dziwani kuti ndidzakudalitsani m’chaka cha 6, ndipo dzikolo lidzakupatsani chakudya cha zaka zitatu.+