-
2 Mbiri 31:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Iye anali kuyang’anira Edeni, Miniyamini, Yesuwa, Semaya, Amariya ndi Sekaniya, m’mizinda ya ansembe+ amene anali pa maudindo awo chifukwa cha kukhulupirika kwawo.+ Amenewa ankagwira ntchito yogawa zinthu kwa abale awo amene anali m’magulu.+ Ankawagawira zinthuzo mofanana, kaya akhale wamkulu kapena wamng’ono.+
-