2 Mafumu 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Bwerera, kauze Hezekiya mtsogoleri+ wa anthu anga kuti, ‘Yehova Mulungu+ wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva+ pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Ndikuchiritsa.+ Pa tsiku lachitatu udzapita kunyumba ya Yehova.+ Yesaya 38:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Yehova analankhula+ ndi Yesaya kuti:
5 “Bwerera, kauze Hezekiya mtsogoleri+ wa anthu anga kuti, ‘Yehova Mulungu+ wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva+ pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Ndikuchiritsa.+ Pa tsiku lachitatu udzapita kunyumba ya Yehova.+