2 Mafumu 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawiyi, Hezekiya anafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro chakuti Yehova andichiritsa, ndi kuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu n’chiyani?”+ Yesaya 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichititsa mthunzi wa dzuwa+ umene wapita kale kutsogolo pamasitepe a Ahazi, kuti ubwerere m’mbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera m’mbuyo pang’onopang’ono masitepe 10 pa masitepe pomwe linali litapita kale kutsogolo.+
8 Pa nthawiyi, Hezekiya anafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro chakuti Yehova andichiritsa, ndi kuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu n’chiyani?”+
8 Ndichititsa mthunzi wa dzuwa+ umene wapita kale kutsogolo pamasitepe a Ahazi, kuti ubwerere m’mbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera m’mbuyo pang’onopang’ono masitepe 10 pa masitepe pomwe linali litapita kale kutsogolo.+