2 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+
22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+