2 Mbiri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuwonjezera apo, analimbitsanso malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ n’kuikamo atsogoleri.+ Atatero m’mizindamo anaikamo chakudya, mafuta ndi vinyo. 2 Mbiri 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’mizinda yonse yosiyanasiyana anaikamo zishango zazikulu+ ndi mikondo ing’onoing’ono.+ Mizindayo anailimbitsa kwambiri, ndipo iye anapitiriza kulamulira Yuda ndi Benjamini.
11 Kuwonjezera apo, analimbitsanso malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ n’kuikamo atsogoleri.+ Atatero m’mizindamo anaikamo chakudya, mafuta ndi vinyo.
12 M’mizinda yonse yosiyanasiyana anaikamo zishango zazikulu+ ndi mikondo ing’onoing’ono.+ Mizindayo anailimbitsa kwambiri, ndipo iye anapitiriza kulamulira Yuda ndi Benjamini.