2 Mbiri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anawauza kuti: “Tamverani Alevi inu. Dziyeretseni+ ndipo muyeretsenso nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu. Mutulutse chinthu chodetsedwa m’malo oyera.+ Ezara 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa chakuti ansembe ndi Alevi anadziyeretsa+ monga gulu limodzi, onse anali oyera. Choncho Aleviwo anapha nyama ya pasika+ ya anthu onse amene anachokera ku ukapolo, ya abale awo ansembe, ndiponso yawo.
5 Ndiyeno anawauza kuti: “Tamverani Alevi inu. Dziyeretseni+ ndipo muyeretsenso nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu. Mutulutse chinthu chodetsedwa m’malo oyera.+
20 Chifukwa chakuti ansembe ndi Alevi anadziyeretsa+ monga gulu limodzi, onse anali oyera. Choncho Aleviwo anapha nyama ya pasika+ ya anthu onse amene anachokera ku ukapolo, ya abale awo ansembe, ndiponso yawo.