1 Mbiri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri. 1 Mbiri 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa magulu a alonda a pazipatawa, ntchito ya atsogoleri awo inali yofanana ndi ya abale awo,+ ndipo inali yotumikira panyumba ya Yehova.
17 Alonda a pazipata+ anali Salumu,+ Akubu, Talimoni, ndi Ahimani. Salumu m’bale wawo ndiye anali mtsogoleri.
12 Pa magulu a alonda a pazipatawa, ntchito ya atsogoleri awo inali yofanana ndi ya abale awo,+ ndipo inali yotumikira panyumba ya Yehova.