1 Mafumu 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mfumukaziyo inafika ku Yerusalemu ndi anthu ambiri oiperekeza.+ Inabwera ndi ngamila+ zitanyamula mafuta a basamu,+ golide wambiri, ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo n’kuyamba kunena zonse zimene zinali kumtima kwake.+ Miyambo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mphatso ndiyo mwala wamtengo wapatali m’maso mwa mwiniwake wolemekezeka.+ Kulikonse kumene amapita zinthu zimamuyendera bwino.+
2 Mfumukaziyo inafika ku Yerusalemu ndi anthu ambiri oiperekeza.+ Inabwera ndi ngamila+ zitanyamula mafuta a basamu,+ golide wambiri, ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo n’kuyamba kunena zonse zimene zinali kumtima kwake.+
8 Mphatso ndiyo mwala wamtengo wapatali m’maso mwa mwiniwake wolemekezeka.+ Kulikonse kumene amapita zinthu zimamuyendera bwino.+