1 Mafumu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zombo+ za Hiramu zimene zinabweretsa golide kuchokera ku Ofiri,+ zinabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ochuluka zedi ndi miyala yamtengo wapatali.+
11 Zombo+ za Hiramu zimene zinabweretsa golide kuchokera ku Ofiri,+ zinabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ochuluka zedi ndi miyala yamtengo wapatali.+