2 Mbiri 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuwonjezera pamenepo, atumiki a Hiramu+ ndi atumiki a Solomo amene anabwera ndi golide+ kuchokera ku Ofiri, anabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ndi miyala yamtengo wapatali.+
10 Kuwonjezera pamenepo, atumiki a Hiramu+ ndi atumiki a Solomo amene anabwera ndi golide+ kuchokera ku Ofiri, anabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ndi miyala yamtengo wapatali.+