8 Sabata lililonse azikhazika mkatewo pamaso pa Yehova, ndipo uzikhala pamenepo nthawi zonse.+ Limeneli ndi pangano pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale.
4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+