Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.

  • 1 Mafumu 10:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 osawerengera golide wochokera kwa amalonda oyendayenda, ndi phindu lochokera kwa amalonda, komanso golide wochokera kwa mafumu onse+ a Aluya,+ ndi kwa abwanamkubwa a m’dzikolo.

  • Yesaya 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Khalani chete inu anthu okhala m’mphepete mwa nyanja. Amalonda a ku Sidoni,+ amene amawoloka nyanja, akulemeretsani.

  • Yesaya 45:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova wanena kuti: “Antchito osalipidwa a ku Iguputo,+ amalonda a ku Itiyopiya, ndi Asabeya,+ amuna ataliatali,+ adzabwera kwa iwe ndipo adzakhala ako.+ Iwo adzayenda pambuyo pako. Adzabwera kwa iwe atamangidwa m’matangadza+ ndipo adzakugwadira.+ Adzapemphera kwa iwe kuti, ‘Zoonadi Mulungu ali ndi iwe+ ndipo palibenso wina. Palibenso Mulungu wina.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena