2 Mbiri 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 osawerengera golide wa amalonda oyendayenda,+ amalonda ena amene anali kubweretsa katundu, mafumu onse a Aluya,+ ndi abwanamkubwa a m’dzikolo amene anali kubweretsa golide ndi siliva kwa Solomo. Salimo 72:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+
14 osawerengera golide wa amalonda oyendayenda,+ amalonda ena amene anali kubweretsa katundu, mafumu onse a Aluya,+ ndi abwanamkubwa a m’dzikolo amene anali kubweretsa golide ndi siliva kwa Solomo.
10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+