2 Mbiri 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova monga anachitira a m’nyumba ya Ahabu, chifukwa iwowo anakhala alangizi+ ake pambuyo pa imfa ya bambo ake, ndipo anam’pweteketsa. Miyambo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Maganizo a anthu olungama ndiwo chilungamo.+ Utsogoleri wa anthu oipa ndi wachinyengo.+
4 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova monga anachitira a m’nyumba ya Ahabu, chifukwa iwowo anakhala alangizi+ ake pambuyo pa imfa ya bambo ake, ndipo anam’pweteketsa.