2 Mbiri 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’kupita kwa nthawi iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo n’kuyamba kutumikira mizati yopatulika+ ndiponso mafano.+ Chotero mkwiyo wa Mulungu unagwera Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kupalamula kwawoko.+ Miyambo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wanga, ochimwa akayesa kukunyengerera usavomere.+ Miyambo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Maganizo a anthu olungama ndiwo chilungamo.+ Utsogoleri wa anthu oipa ndi wachinyengo.+ Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
18 M’kupita kwa nthawi iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo n’kuyamba kutumikira mizati yopatulika+ ndiponso mafano.+ Chotero mkwiyo wa Mulungu unagwera Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kupalamula kwawoko.+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+