Miyambo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wosonyeza kukoma mtima kosatha amapindulitsa moyo wake,+ koma munthu wankhanza amachititsa kuti thupi lake linyanyalidwe.+ Mlaliki 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuponderezedwa kumapangitsa munthu wanzeru kuchita zinthu zopanda nzeru,+ ndipo mphatso+ ikhoza kuwononga mtima wa munthu.+
17 Munthu wosonyeza kukoma mtima kosatha amapindulitsa moyo wake,+ koma munthu wankhanza amachititsa kuti thupi lake linyanyalidwe.+
7 Kuponderezedwa kumapangitsa munthu wanzeru kuchita zinthu zopanda nzeru,+ ndipo mphatso+ ikhoza kuwononga mtima wa munthu.+