Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mizinda yonseyi inali ya mipanda yolimba kwambiri ndiponso yaitali, yokhala ndi zitseko ndi mipiringidzo. Kuwonjezera pamenepo, tinalandanso matauni ambirimbiri akumidzi.

  • Oweruza 16:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma Samisoni anagonabe mpaka pakati pa usiku. Kenako anadzuka pakati pa usikupo ndi kugwira zitseko za chipata cha mzinda+ pamodzi ndi nsanamira zake ziwiri, n’kuzizula pamodzi ndi mpiringidzo wake. Atatero anazinyamula pamapewa+ n’kupita nazo pamwamba pa phiri limene lili moyang’anana ndi Heburoni.+

  • 1 Samueli 23:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Patapita nthawi, Sauli analandira uthenga wonena kuti: “Davide ali ku Keila.”+ Pamenepo Sauli ananena kuti: “Mulungu wamugulitsa kwa ine,+ pakuti wadzitsekera yekha mwa kulowa mumzinda wokhala ndi zitseko ndi mipiringidzo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena